Salimo 91:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sudzaopa mliri umene umayenda mu mdima,+Kapena chiwonongeko chimene chimachitika dzuwa lili paliwombo.+ Yeremiya 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+
6 Sudzaopa mliri umene umayenda mu mdima,+Kapena chiwonongeko chimene chimachitika dzuwa lili paliwombo.+
8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+