Yesaya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masana ukhoza kuumangira mpanda wabwino munda wakowo, ndipo m’mawa ukhoza kuchititsa mbewu yako kuti iphuke. Koma zokolola zake zidzathawa m’tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+ Hoseya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+
11 Masana ukhoza kuumangira mpanda wabwino munda wakowo, ndipo m’mawa ukhoza kuchititsa mbewu yako kuti iphuke. Koma zokolola zake zidzathawa m’tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+
7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+