Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndimuuza Mulungu kuti, ‘Musanene kuti ndine woipa.

      Ndiuzeni chifukwa chimene mukulimbanirana nane.

  • 1 Akorinto 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Koma ngati tingazindikire mmene tilili, sitingaweruzidwe.+

  • Yakobo 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi nkhondo zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Nanga kukangana pakati panu kukuchokera kuti? Kodi sizikuchokera m’zilakolako za thupi lanu+ zimene zikuchita nkhondo m’ziwalo zanu?+

  • Chivumbulutso 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena