Oweruza 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mtengo wa maoliviwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kutulutsa mafuta amene amagwiritsidwa ntchito potamanda+ Mulungu ndi anthu, n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’+ Zekariya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinafunsa mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja kuti: “Kodi mitengo iwiri ya maolivi, imene wina uli kudzanja lamanja ndi wina kumanzere kwa choikapo nyalechi, ikuimira chiyani?”+ Chivumbulutso 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi,+ ndi zoikapo nyale ziwiri,+ ndipo mbonizo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+
9 Koma mtengo wa maoliviwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kutulutsa mafuta amene amagwiritsidwa ntchito potamanda+ Mulungu ndi anthu, n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’+
11 Ndiyeno ndinafunsa mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja kuti: “Kodi mitengo iwiri ya maolivi, imene wina uli kudzanja lamanja ndi wina kumanzere kwa choikapo nyalechi, ikuimira chiyani?”+
4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi,+ ndi zoikapo nyale ziwiri,+ ndipo mbonizo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+