Mlaliki 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ineyo ndinadana ndi ntchito yonse yovuta imene ndinali kugwira padziko lapansi pano,+ imene ndidzasiyire munthu amene akubwera pambuyo panga.+ Amosi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi+ pamodzi ndi wogwira ndodo yachifumu wa ku Asikeloni.+ Ndidzalanga+ Ekironi+ ndipo ndidzafafaniza otsala mwa Afilisiti,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’
18 Ineyo ndinadana ndi ntchito yonse yovuta imene ndinali kugwira padziko lapansi pano,+ imene ndidzasiyire munthu amene akubwera pambuyo panga.+
8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi+ pamodzi ndi wogwira ndodo yachifumu wa ku Asikeloni.+ Ndidzalanga+ Ekironi+ ndipo ndidzafafaniza otsala mwa Afilisiti,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’