Ezekieli 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nkhosa zodwala simunazilimbitse+ ndipo zamatenda simunazichiritse. Yothyoka mwendo simunaimange mwendo wothyokawo. Nkhosa zomwazika simunazibweze ndipo zosochera simunazifufuze kuti muzipeze.+ Munali kuzilamulira mouma mtima komanso mwankhanza.+
4 Nkhosa zodwala simunazilimbitse+ ndipo zamatenda simunazichiritse. Yothyoka mwendo simunaimange mwendo wothyokawo. Nkhosa zomwazika simunazibweze ndipo zosochera simunazifufuze kuti muzipeze.+ Munali kuzilamulira mouma mtima komanso mwankhanza.+