Ekisodo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Gerisoni anali Libini ndi Simeyi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ 1 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya. 1 Mbiri 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Simeyi anali Yahati, Zina,* Yeusi, ndi Beriya. Ana anayiwa anali a Simeyi.
8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.