Deuteronomo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Uziiwotcha ndi kuidya+ pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe,+ ndipo m’mawa mwake uzitembenuka ndi kubwerera kumahema ako. 1 Samueli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, pamene nyama imeneyi inali kuwira, mtumiki wa wansembe anali kubwera ndi foloko ya mano atatu m’manja mwake.+ Ezekieli 46:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Panali kakhoma kamiyala kuzungulira mkati monse mwa tinyumba tonse tinayi tapakonato. M’munsi monse mwa kakhoma kameneko munali malo ophikirapo.+
7 Uziiwotcha ndi kuidya+ pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe,+ ndipo m’mawa mwake uzitembenuka ndi kubwerera kumahema ako.
13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, pamene nyama imeneyi inali kuwira, mtumiki wa wansembe anali kubwera ndi foloko ya mano atatu m’manja mwake.+
23 Panali kakhoma kamiyala kuzungulira mkati monse mwa tinyumba tonse tinayi tapakonato. M’munsi monse mwa kakhoma kameneko munali malo ophikirapo.+