Salimo 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Gonjerani anthu inu, ndipo dziwani kuti ine ndine Mulungu.+Ndidzakwezedwa pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndidzakwezedwa padziko lapansi.”+ Habakuku 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+ Inu anthu onse a padziko lapansi, khalani chete pamaso pake!’”+ Zefaniya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.
10 “Gonjerani anthu inu, ndipo dziwani kuti ine ndine Mulungu.+Ndidzakwezedwa pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndidzakwezedwa padziko lapansi.”+
20 Koma Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+ Inu anthu onse a padziko lapansi, khalani chete pamaso pake!’”+
7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.