Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu. Salimo 115:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Mulungu wathu ali kumwamba.+Chilichonse chimene anafuna kuchita anachita.+ Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+ Aheberi 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi wantchito wotumikira ena wa m’malo oyerawo+ komanso m’chihema chenicheni, chomangidwa ndi Yehova,+ osati munthu.+
4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.
6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+
2 Iye ndi wantchito wotumikira ena wa m’malo oyerawo+ komanso m’chihema chenicheni, chomangidwa ndi Yehova,+ osati munthu.+