Deuteronomo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 iyenso* adzakupatsani mvula pa nthawi yake m’dziko lanu,+ mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza,+ ndipo mudzakololadi mbewu zanu ndi kukhaladi ndi vinyo wotsekemera* komanso mafuta. Yoweli 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Malo opunthira mbewu adzadzaza ndi mbewu zopunthidwa ndipo malo ogweramo vinyo watsopano ndi mafuta adzasefukira.+ Zekariya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘M’dzikolo mudzakhala mbewu ya mtendere.+ Mpesa udzabala zipatso+ ndipo dziko lapansi lidzapereka zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ake.+ Ndidzachititsa kuti anthu otsala+ mwa anthu awa adzalandire zinthu zonsezi.+
14 iyenso* adzakupatsani mvula pa nthawi yake m’dziko lanu,+ mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza,+ ndipo mudzakololadi mbewu zanu ndi kukhaladi ndi vinyo wotsekemera* komanso mafuta.
24 Malo opunthira mbewu adzadzaza ndi mbewu zopunthidwa ndipo malo ogweramo vinyo watsopano ndi mafuta adzasefukira.+
12 ‘M’dzikolo mudzakhala mbewu ya mtendere.+ Mpesa udzabala zipatso+ ndipo dziko lapansi lidzapereka zokolola zake.+ Kumwamba kudzagwetsa mame ake.+ Ndidzachititsa kuti anthu otsala+ mwa anthu awa adzalandire zinthu zonsezi.+