Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+ Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+
9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+