Salimo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+ Yesaya 59:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo, ndipo iwo sadzavala zochita zawo.+ Ntchito zawo n’zopweteka ena, ndipo m’manja mwawo muli ntchito zachiwawa.+
5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+
6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo, ndipo iwo sadzavala zochita zawo.+ Ntchito zawo n’zopweteka ena, ndipo m’manja mwawo muli ntchito zachiwawa.+