Maliko 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi ina Yesu anali kudya patebulo m’nyumba ya Levi, ndipo okhometsa msonkho+ ndi ochimwa ambiri anali kudya pamodzi ndi iye ndi ophunzira ake. Kumeneko kunali anthu ambiri ndipo anayamba kumutsatira.+
15 Pa nthawi ina Yesu anali kudya patebulo m’nyumba ya Levi, ndipo okhometsa msonkho+ ndi ochimwa ambiri anali kudya pamodzi ndi iye ndi ophunzira ake. Kumeneko kunali anthu ambiri ndipo anayamba kumutsatira.+