Mateyu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi inayake, pamene anali kudya patebulo m’nyumba ina,+ kunabwera okhometsa msonkho ndi ochimwa ambiri ndipo anayamba kudya pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake. Luka 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano Levi anakonzera Yesu phwando lalikulu kunyumba kwake. Kumeneko kunali khamu lalikulu la okhometsa msonkho ndi ena ambiri, ndipo anali kudyera limodzi.+
10 Nthawi inayake, pamene anali kudya patebulo m’nyumba ina,+ kunabwera okhometsa msonkho ndi ochimwa ambiri ndipo anayamba kudya pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ake.
29 Tsopano Levi anakonzera Yesu phwando lalikulu kunyumba kwake. Kumeneko kunali khamu lalikulu la okhometsa msonkho ndi ena ambiri, ndipo anali kudyera limodzi.+