Maliko 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ataona zimenezi Afarisiwo anatuluka ndipo nthawi yomweyo anapita kukakonza chiwembu limodzi ndi a chipani cha Herode+ kuti amuphe.+ Maliko 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake anam’tumizira ena mwa Afarisi ndi a chipani cha Herode,+ kuti akam’kole m’mawu ake.+
6 Ataona zimenezi Afarisiwo anatuluka ndipo nthawi yomweyo anapita kukakonza chiwembu limodzi ndi a chipani cha Herode+ kuti amuphe.+