Mateyu 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+ Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+ Luka 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+ Yohane 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+ Yohane 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Anasi anatumiza Yesu ali womangidwa kwa Kayafa mkulu wa ansembe.+
57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+
2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+
2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+
13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+