Luka 22:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pamenepo anamugwira ndi kumutenga,+ ndipo anakamulowetsa m’nyumba ya mkulu wa ansembe.+ Koma Petulo anali kuwatsatira chapatali.+
54 Pamenepo anamugwira ndi kumutenga,+ ndipo anakamulowetsa m’nyumba ya mkulu wa ansembe.+ Koma Petulo anali kuwatsatira chapatali.+