Mateyu 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+ Yohane 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+ Yohane 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Anasi anatumiza Yesu ali womangidwa kwa Kayafa mkulu wa ansembe.+ Machitidwe 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 (Pamenepo panalinso Anasi+ wansembe wamkulu, Kayafa,+ Yohane, Alekizanda, ndi achibale ambiri a wansembe wamkuluyo.)
57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+
13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+
6 (Pamenepo panalinso Anasi+ wansembe wamkulu, Kayafa,+ Yohane, Alekizanda, ndi achibale ambiri a wansembe wamkuluyo.)