Mateyu 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+ Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+ Yohane 11:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Koma mmodzi wa iwo, Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho,+ anati: “Palibe chimene mukudziwa inu,
57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+
2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+
49 Koma mmodzi wa iwo, Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho,+ anati: “Palibe chimene mukudziwa inu,