Maliko 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano anabwerera ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Simoni, zoona ukugona? Kodi unalibe mphamvu kuti ukanakhalabe maso ola limodzi?+ Luka 22:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako ananyamuka pamene anali kupemphererapo n’kupita kwa ophunzira aja. Koma anawapeza atagona chifukwa cha chisoni.+
37 Tsopano anabwerera ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Simoni, zoona ukugona? Kodi unalibe mphamvu kuti ukanakhalabe maso ola limodzi?+
45 Kenako ananyamuka pamene anali kupemphererapo n’kupita kwa ophunzira aja. Koma anawapeza atagona chifukwa cha chisoni.+