Mateyu 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atatero anabwerera pamene panali ophunzira ake aja ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Zoona anthu inu simungathe kukhalabe maso limodzi ndi ine ola limodzi?+ Luka 22:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako ananyamuka pamene anali kupemphererapo n’kupita kwa ophunzira aja. Koma anawapeza atagona chifukwa cha chisoni.+
40 Atatero anabwerera pamene panali ophunzira ake aja ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Zoona anthu inu simungathe kukhalabe maso limodzi ndi ine ola limodzi?+
45 Kenako ananyamuka pamene anali kupemphererapo n’kupita kwa ophunzira aja. Koma anawapeza atagona chifukwa cha chisoni.+