Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+ Yohane 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumeneko anamupachika+ pamodzi ndi amuna ena awiri, wina mbali iyi, wina mbali inayi, Yesu pakati.+
16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+
18 Kumeneko anamupachika+ pamodzi ndi amuna ena awiri, wina mbali iyi, wina mbali inayi, Yesu pakati.+