Maliko 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu ataona chikhulupiriro chawo,+ anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Mwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+ Maliko 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chapafupi n’chiti, kuuza wakufa ziwaloyu kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Nyamuka ndipo nyamula machira ako uyende’?+ Luka 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ataona chikhulupiriro chawo, anati: “Bwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+
5 Yesu ataona chikhulupiriro chawo,+ anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Mwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+
9 Chapafupi n’chiti, kuuza wakufa ziwaloyu kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Nyamuka ndipo nyamula machira ako uyende’?+