38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+
26 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi akadzafika mu ulemerero wake, wa Atate wake ndi wa angelo oyera.+