Mateyu 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma aliyense wondikana ine pamaso pa anthu, inenso ndidzamukana+ pamaso pa Atate wanga wakumwamba. Maliko 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+ 2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,
33 Koma aliyense wondikana ine pamaso pa anthu, inenso ndidzamukana+ pamaso pa Atate wanga wakumwamba.
38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+
12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,