Mateyu 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse. Mateyu 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, anachoka ku Galileya ndi kubwera kumadera a kumalire kwa Yudeya kutsidya la Yorodano.+ Luka 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo ananyamuka ndi kulowa m’deralo m’mudzi ndi mudzi. Iwo anali kulengeza uthenga wabwino ndi kuchiritsa anthu kwina kulikonse.+
23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse.
19 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, anachoka ku Galileya ndi kubwera kumadera a kumalire kwa Yudeya kutsidya la Yorodano.+
6 Pamenepo ananyamuka ndi kulowa m’deralo m’mudzi ndi mudzi. Iwo anali kulengeza uthenga wabwino ndi kuchiritsa anthu kwina kulikonse.+