Mateyu 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma iye anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita mantha chonchi, anthu achikhulupiriro chochepa inu?”+ Kenako anadzuka n’kudzudzula mphepo ndi nyanjayo, ndipo panachita bata lalikulu.+ Maliko 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu poona zimenezo, anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana nkhani yosowa mikate?+ Kodi simukuzindikira ndi kumvetsa tanthauzo lake mpaka pano? Kodi mitima yanu ikadali yosazindikira?+
26 Koma iye anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita mantha chonchi, anthu achikhulupiriro chochepa inu?”+ Kenako anadzuka n’kudzudzula mphepo ndi nyanjayo, ndipo panachita bata lalikulu.+
17 Yesu poona zimenezo, anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana nkhani yosowa mikate?+ Kodi simukuzindikira ndi kumvetsa tanthauzo lake mpaka pano? Kodi mitima yanu ikadali yosazindikira?+