Salimo 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+ Salimo 89:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyanja ikadzaza mumailamulira.+Mafunde ake akamawinduka, inuyo mumawakhalitsa bata.+ Salimo 107:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amachititsa mphepo yamkuntho kukhala bata,+Moti mafunde a panyanja amadekha.+ Luka 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Chikhulupiriro chanu chili kuti?” Koma iwo anagwidwa ndi mantha ndipo anathedwa nzeru, mwakuti anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, wochita kulamula mphepo ndi madzi ndipo n’kumumvera?”+
7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+
25 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Chikhulupiriro chanu chili kuti?” Koma iwo anagwidwa ndi mantha ndipo anathedwa nzeru, mwakuti anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, wochita kulamula mphepo ndi madzi ndipo n’kumumvera?”+