Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Atadziwa zimenezi, Yesu anatuluka mmenemo. Anthu ambiri anam’tsatira ndipo iye anawachiritsa onsewo,+

  • Luka 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako anatsika nawo ndi kuima pamalo am’munsi, athyathyathya. Pamenepo panali khamu lalikulu la ophunzira ake. Panalinso chikhamu cha anthu+ ochokera ku Yudeya konse ndi ku Yerusalemu konse, komanso kumadera am’mphepete mwa nyanja a ku Turo ndi ku Sidoni. Onsewo anabwera kudzamumvetsera ndi kudzachiritsidwa matenda awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena