Mateyu 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ali mkati molankhula ndi khamu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi abale ake.+ Iwo anaima panja kufuna kuti alankhule naye. Luka 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano mayi ake ndi abale ake+ anabwera kumeneko, koma chifukwa cha khamu la anthu, analephera kufika kumene iyeyo anali.+
46 Ali mkati molankhula ndi khamu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi abale ake.+ Iwo anaima panja kufuna kuti alankhule naye.
19 Tsopano mayi ake ndi abale ake+ anabwera kumeneko, koma chifukwa cha khamu la anthu, analephera kufika kumene iyeyo anali.+