Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?

  • Maliko 3:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsopano panafika mayi ake ndi abale ake,+ ndipo anaimirira kunja, ndi kutumiza mthenga kukamuitana.+

  • Yohane 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Izi zitatha, iye, mayi ake, abale ake+ ndi ophunzira ake anapita ku Kaperenao,+ koma kumeneko sanakhaleko masiku ambiri.

  • Machitidwe 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mogwirizana, onsewa analimbikira kupemphera,+ pamodzi ndi amayi ena+ komanso Mariya mayi a Yesu, limodzinso ndi abale ake a Yesu.+

  • 1 Akorinto 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tili ndi ufulu wotenga alongo amene ndi akazi athu+ pa maulendo, mmene amachitira atumwi ena onse ndiponso abale a Ambuye+ komanso Kefa,+ si choncho kodi?

  • Agalatiya 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma sindinaone mtumwi winanso kupatulapo Yakobo,+ m’bale+ wa Ambuye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena