Mateyu 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso mbewu zina zinagwera paminga, ndipo mingazo zinakula ndi kulepheretsa mbewuzo kukula.+ Maliko 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno palinso mbewu zina zofesedwa paminga. Zimenezi ndiwo anthu amene amamva mawu,+ Maliko 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 koma nkhawa+ za m’nthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma,+ komanso zilakolako+ za zinthu zina, zimalowa ndi kulepheretsa mawuwo kukula, ndipo sabala zipatso.+ Luka 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zinanso zinagwera paminga. Mingazo zinali kukulira limodzi ndi mbewuzo ndipo zinalepheretsa mbewuzo kukula.+
19 koma nkhawa+ za m’nthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma,+ komanso zilakolako+ za zinthu zina, zimalowa ndi kulepheretsa mawuwo kukula, ndipo sabala zipatso.+
7 Zinanso zinagwera paminga. Mingazo zinali kukulira limodzi ndi mbewuzo ndipo zinalepheretsa mbewuzo kukula.+