Mateyu 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano atalowa m’nyumba ya wolamulira uja,+ anaona oliza zitoliro komanso khamu la anthu likubuma.+ Luka 8:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma anthu onse anali kulira ndi kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ pakuti mwanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Yohane 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+
23 Tsopano atalowa m’nyumba ya wolamulira uja,+ anaona oliza zitoliro komanso khamu la anthu likubuma.+
52 Koma anthu onse anali kulira ndi kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ pakuti mwanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+
11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+