Mateyu 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anayankha kuti: “Ena akumanena kuti Yohane M’batizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akuti Yeremiya kapena mmodzi wa aneneri.” Luka 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Poyankha iwo anati: “Amati ndinu Yohane M’batizi. Koma ena amati ndinu Eliya. Enanso amati mmodzi wa aneneri akale wauka.”+
14 Iwo anayankha kuti: “Ena akumanena kuti Yohane M’batizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akuti Yeremiya kapena mmodzi wa aneneri.”
19 Poyankha iwo anati: “Amati ndinu Yohane M’batizi. Koma ena amati ndinu Eliya. Enanso amati mmodzi wa aneneri akale wauka.”+