Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni sangalala kwambiri.+ Fuula mokondwera+ iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu. Taona, mfumu yako+ ikubwera kwa iwe.+ Mfumuyo ndi yolungama ndipo yapambana.+ Iyo ndi yodzichepetsa+ ndipo ikubwera itakwera bulu. Ikubwera itakwera nyama yokhwima, imene ndi mwana wamphongo wa bulu.+

  • Luka 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+

  • Machitidwe 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Amuna inu, abale anga, ndilankhula ndithu mwaufulu za kholo lathu Davide. Iye anamwalira+ ndi kuikidwa m’manda, ndipo manda ake tili nawo mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena