Mika 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+ Mateyu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+ Luka 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso makolo anu enieniwo,+ abale anu, anthu oyandikana nanu ndi mabwenzi anu, adzakuperekani, ndipo adzapha ena a inu.+ 2 Timoteyo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+
6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+
21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+
16 Komanso makolo anu enieniwo,+ abale anu, anthu oyandikana nanu ndi mabwenzi anu, adzakuperekani, ndipo adzapha ena a inu.+
3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+