Mateyu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+ Luka 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo . . .” anauza munthu wakufa ziwalo uja kuti: “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+
6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+
24 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo . . .” anauza munthu wakufa ziwalo uja kuti: “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+