Mateyu 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero ophunzirawo anachitadi monga mmene Yesu anawalamulira, ndipo anakonza zinthu zonse zofunika pa pasika.+ Maliko 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ophunzirawo anapita ndi kulowa mumzinda, ndipo zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Chotero anakonzekera pasika kumeneko.+ Luka 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho otumidwawo ananyamuka ndipo anakam’pezadi mmene iye anawauzira.+
19 Chotero ophunzirawo anachitadi monga mmene Yesu anawalamulira, ndipo anakonza zinthu zonse zofunika pa pasika.+
16 Choncho ophunzirawo anapita ndi kulowa mumzinda, ndipo zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Chotero anakonzekera pasika kumeneko.+