Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+

  • Mateyu 27:62
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Tsiku lotsatira, pambuyo pa Tsiku Lokonzekera,+ ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhana pamaso pa Pilato,

  • Maliko 15:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Tsopano madzulo, popeza linali Tsiku Lokonzekera, kapena kuti tsiku loti m’mawa mwake ndi sabata,

  • Yohane 19:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Choncho, popeza linali tsiku lokonzekera+ chikondwerero cha Ayuda, iwo anaika Yesu mmenemo, chifukwa manda achikumbutsowo anali pafupi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena