Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+

  • Hoseya 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye adzatikhalitsa ndi moyo pambuyo pa masiku awiri.+ Pa tsiku lachitatu adzatidzutsa ndipo tidzakhalanso ndi moyo pamaso pake. +

  • Yona 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona,+ moti Yona anakhala m’mimba mwa nsomba masiku atatu, usana ndi usiku.+

  • Maliko 9:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pakuti anali kuphunzitsa ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa m’manja mwa anthu, ndipo adzamupha,+ koma ngakhale adzamuphe, adzauka patapita masiku atatu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena