Luka 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Zakeyu anaimirira ndi kuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense pomunamizira mlandu+ ndibweza kuwirikiza kanayi.”+ 1 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akuba, aumbombo,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+
8 Koma Zakeyu anaimirira ndi kuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense pomunamizira mlandu+ ndibweza kuwirikiza kanayi.”+