Mateyu 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba m’nyanja, pakuti anali asodzi. Mayina awo anali Simoni+ wotchedwa Petulo+ ndi Andireya. Maliko 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya* Yesu anaona Simoni+ ndi Andireya m’bale wake wa Simoni, akuponya maukonde awo m’nyanjamo, pakuti anali asodzi.+
18 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba m’nyanja, pakuti anali asodzi. Mayina awo anali Simoni+ wotchedwa Petulo+ ndi Andireya.
16 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya* Yesu anaona Simoni+ ndi Andireya m’bale wake wa Simoni, akuponya maukonde awo m’nyanjamo, pakuti anali asodzi.+