Mateyu 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma poona zimenezi, Afarisi anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani mphunzitsi wanu amadya limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+ Maliko 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma alembi a Afarisi, ataona kuti iye akudya limodzi ndi anthu ochimwa ndi okhometsa msonkho, anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “Bwanji akudya limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+ Luka 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afarisi ndi alembi ataona zimenezi anayamba kung’ung’udza kuti: “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa ndi kudya nawo limodzi.”+
11 Koma poona zimenezi, Afarisi anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani mphunzitsi wanu amadya limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+
16 Koma alembi a Afarisi, ataona kuti iye akudya limodzi ndi anthu ochimwa ndi okhometsa msonkho, anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “Bwanji akudya limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+
2 Afarisi ndi alembi ataona zimenezi anayamba kung’ung’udza kuti: “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa ndi kudya nawo limodzi.”+