21 Palibe amene amasokerera chigamba cha nsalu yatsopano pamalaya akunja akale. Ngati wina atachita zimenezi, mphamvu yonse ya chigambacho imakoka ndi kung’amba malayawo. Chigamba chatsopanocho chimang’amba malaya akalewo, ndipo kung’ambikako kumawonjezeka kwambiri.+