Yesaya 58:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kusala kudya kumene ine ndimafuna n’kotere: Mumasule maunyolo ozunzira anzanu,+ mumasule zingwe za goli,+ mumasule anthu opsinjika kuti azipita kwawo,+ ndipo goli lililonse mulithyole pakati.+ Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Maliko 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo mukaimirira n’kumapemphera,+ khululukani chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireni machimo anunso.”+
6 “Kusala kudya kumene ine ndimafuna n’kotere: Mumasule maunyolo ozunzira anzanu,+ mumasule zingwe za goli,+ mumasule anthu opsinjika kuti azipita kwawo,+ ndipo goli lililonse mulithyole pakati.+
25 Ndipo mukaimirira n’kumapemphera,+ khululukani chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireni machimo anunso.”+