Esitere 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuti abweretse Mfumukazi Vasiti itavala duku lachifumu pamaso pa mfumu, kuti anthu onse ndi akalonga aone kuoneka bwino kwake, pakuti inalidi yokongola kwambiri.+ Mateyu 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nanga munapita kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zapamwamba kapena? Iyayi, pajatu ovala zovala zapamwamba amapezeka m’nyumba za mafumu.+
11 kuti abweretse Mfumukazi Vasiti itavala duku lachifumu pamaso pa mfumu, kuti anthu onse ndi akalonga aone kuoneka bwino kwake, pakuti inalidi yokongola kwambiri.+
8 Nanga munapita kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zapamwamba kapena? Iyayi, pajatu ovala zovala zapamwamba amapezeka m’nyumba za mafumu.+