Miyambo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wabwino Yehova amakondwera naye,+ koma munthu wamaganizo oipa iye amamutcha woipa.+