Deuteronomo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+ 1 Mafumu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+ Yesaya 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wopusa sadzatchedwanso wopatsa, ndipo munthu wopanda khalidwe sadzatchedwa wolemekezeka,+
25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+
32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+