Salimo 112:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi munthu wotero sadzagwedezeka ngakhale pang’ono.+ ל [Laʹmedh]Wolungama adzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ Miyambo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amanyansidwa ndi njira ya munthu woipa,+ koma iye amakonda munthu wochita chilungamo.+
6 Ndithudi munthu wotero sadzagwedezeka ngakhale pang’ono.+ ל [Laʹmedh]Wolungama adzakumbukiridwa mpaka kalekale.+